Numeri 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aziperekanso dengu la mikate yozungulira yoboola pakati yopanda zofufumitsa, yophika ndi ufa wosalala ndi yopaka mafuta, timikate topyapyala topanda zofufumitsa topaka mafuta, limodzi ndi nsembe yake yambewu+ ndiponso nsembe zake zachakumwa.+
15 Aziperekanso dengu la mikate yozungulira yoboola pakati yopanda zofufumitsa, yophika ndi ufa wosalala ndi yopaka mafuta, timikate topyapyala topanda zofufumitsa topaka mafuta, limodzi ndi nsembe yake yambewu+ ndiponso nsembe zake zachakumwa.+