-
Numeri 6:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Wansembeyo azibweretsa zinthuzo pamaso pa Yehova, ndipo azimuperekera nsembe yake yamachimo ndi nsembe yake yopsereza.
-