Numeri 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mnaziriyo azimeta tsitsi lakumutu kwake+ ndipo azimetera pakhomo la chihema chokumanako. Akatero, azitenga tsitsi lakumutu kwake limene linamera pa nthawi yomwe anali Mnaziri, nʼkuliponya pamoto umene uli pansi pa nsembe yamgwirizano.
18 Kenako Mnaziriyo azimeta tsitsi lakumutu kwake+ ndipo azimetera pakhomo la chihema chokumanako. Akatero, azitenga tsitsi lakumutu kwake limene linamera pa nthawi yomwe anali Mnaziri, nʼkuliponya pamoto umene uli pansi pa nsembe yamgwirizano.