-
Numeri 6:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Wansembeyo aziyendetsa zinthuzo uku ndi uku monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova.+ Zinthuzi ziziperekedwa kwa wansembeyo ngati mphatso yopatulika, limodzi ndi chidale cha nsembe yoyendetsa uku ndi uku, komanso mwendo womwe ndi gawo lopatulika.+ Pambuyo pake munthu yemwe anali Mnaziriyo angathe kumwa vinyo.
-