Numeri 7:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Potsegulira guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri a Isiraeli anapereka izi:+ Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva 12 ndi makapu agolide 12.+
84 Potsegulira guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri a Isiraeli anapereka izi:+ Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva 12 ndi makapu agolide 12.+