Numeri 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Aroni anachita izi: Anayatsa nyalezo kuti ziunikire malo apatsogolo pa choikapo nyalecho,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
3 Choncho Aroni anachita izi: Anayatsa nyalezo kuti ziunikire malo apatsogolo pa choikapo nyalecho,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.