Numeri 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako iwo atenge ngʼombe yaingʼono yamphongo,+ pamodzi ndi nsembe yake yambewu+ ya ufa wosalala wothira mafuta. Iweyo utenge ngʼombe inanso yaingʼono yamphongo ya nsembe yamachimo.+
8 Kenako iwo atenge ngʼombe yaingʼono yamphongo,+ pamodzi ndi nsembe yake yambewu+ ya ufa wosalala wothira mafuta. Iweyo utenge ngʼombe inanso yaingʼono yamphongo ya nsembe yamachimo.+