Numeri 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndi operekedwa. Aperekedwa kwa ine kuchokera pakati pa Aisiraeli. Ine ndikuwatenga kukhala anga mʼmalo mwa onse oyamba kubadwa* pakati pa Aisiraeli.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:16 Nsanja ya Olonda,4/15/1992, tsa. 12
16 Amenewa ndi operekedwa. Aperekedwa kwa ine kuchokera pakati pa Aisiraeli. Ine ndikuwatenga kukhala anga mʼmalo mwa onse oyamba kubadwa* pakati pa Aisiraeli.+