Numeri 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mwana aliyense woyamba kubadwa pakati pa Aisiraeli ndi wanga, kaya akhale wa munthu kapena wa nyama.+ Pa tsiku limene ndinapha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo, ndinawapatula kuti akhale anga.+
17 Mwana aliyense woyamba kubadwa pakati pa Aisiraeli ndi wanga, kaya akhale wa munthu kapena wa nyama.+ Pa tsiku limene ndinapha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo, ndinawapatula kuti akhale anga.+