-
Numeri 8:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mose ndi Aroni ndi gulu lonse la Aisiraeli, anachita zimenezi kwa Aleviwo. Aisiraeliwo anachitira Aleviwo mogwirizana ndi zonse zimene Yehova analamula Mose zokhudza Alevi.
-