Numeri 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼmwezi woyamba wa chaka chachiwiri, Aisiraeli atatuluka mʼdziko la Iguputo, Yehova analankhula ndi Mose mʼchipululu cha Sinai.+ Iye anati:
9 Mʼmwezi woyamba wa chaka chachiwiri, Aisiraeli atatuluka mʼdziko la Iguputo, Yehova analankhula ndi Mose mʼchipululu cha Sinai.+ Iye anati: