Numeri 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 nʼkunena kuti: “Ife ndife odetsedwa chifukwa takhudza munthu wakufa. Ngakhale kuti zili choncho, kodi tikuyeneradi kuletsedwa kupereka nsembe kwa Yehova pakati pa Aisiraeli pa nthawi imene inaikidwiratu?”+
7 nʼkunena kuti: “Ife ndife odetsedwa chifukwa takhudza munthu wakufa. Ngakhale kuti zili choncho, kodi tikuyeneradi kuletsedwa kupereka nsembe kwa Yehova pakati pa Aisiraeli pa nthawi imene inaikidwiratu?”+