Numeri 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Asamasiye nyama iliyonse mpaka mʼmamawa,+ ndipo asamaphwanye fupa lake lililonse.+ Aziikonza motsatira malamulo onse a Pasika.
12 Asamasiye nyama iliyonse mpaka mʼmamawa,+ ndipo asamaphwanye fupa lake lililonse.+ Aziikonza motsatira malamulo onse a Pasika.