Numeri 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yehova akalamula, Aisiraeli ankanyamuka, ndipo Yehova akalamula, ankamanga msasa.+ Masiku onse amene mtambo unkakhala pamwamba pa chihemacho, iwo ankakhalabe pamsasapo.
18 Choncho Yehova akalamula, Aisiraeli ankanyamuka, ndipo Yehova akalamula, ankamanga msasa.+ Masiku onse amene mtambo unkakhala pamwamba pa chihemacho, iwo ankakhalabe pamsasapo.