Numeri 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale mtambowo utakhala masiku ambiri pamwamba pa chihema, Aisiraeli ankamverabe Yehova, ndipo sankachoka pamalopo.+
19 Ngakhale mtambowo utakhala masiku ambiri pamwamba pa chihema, Aisiraeli ankamverabe Yehova, ndipo sankachoka pamalopo.+