-
Numeri 9:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Nthawi zina mtambowo unkangokhala masiku owerengeka pamwamba pa chihemapo. Yehova akalamula, iwo ankakhalabe pamsasapo ndipo Yehova akalamula, iwo ankachokapo.
-