Numeri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nthawi zina mtambowo unkangokhalapo kuchokera madzulo mpaka mʼmamawa, ndipo mtambowo ukachoka mʼmamawawo, anthuwo ankanyamuka. Kaya mtambowo uchoke masana kapena usiku, iwo ankanyamuka.+
21 Nthawi zina mtambowo unkangokhalapo kuchokera madzulo mpaka mʼmamawa, ndipo mtambowo ukachoka mʼmamawawo, anthuwo ankanyamuka. Kaya mtambowo uchoke masana kapena usiku, iwo ankanyamuka.+