-
Numeri 9:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kaya mtambowo ukhale pamwamba pa chihemacho masiku awiri, mwezi, kapena masiku ambiri, Aisiraeli ankakhalabe pamsasa osachoka. Koma mtambowo ukanyamuka, iwo ankachoka.
-