-
Numeri 9:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Yehova akalamula, iwo ankamanga msasa, ndipo Yehova akalamula, iwo ankanyamuka. Ankamvera Yehova potsatira malangizo amene Yehova anapereka kudzera mwa Mose.
-