Numeri 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mukaliza kachiwiri lipenga lolira mosinthasintha, anthu amene ali mʼmisasa yakumʼmwera+ azinyamuka. Gulu lililonse likamanyamuka, aziliza lipenga lolira mosinthasintha.
6 Mukaliza kachiwiri lipenga lolira mosinthasintha, anthu amene ali mʼmisasa yakumʼmwera+ azinyamuka. Gulu lililonse likamanyamuka, aziliza lipenga lolira mosinthasintha.