Numeri 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ana a Aroni, omwe ndi ansembe, ndi amene aziliza malipengawo.+ Ndi lamulo kwa inu kuti muzigwiritsa ntchito malipengawa mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale.
8 Ana a Aroni, omwe ndi ansembe, ndi amene aziliza malipengawo.+ Ndi lamulo kwa inu kuti muzigwiritsa ntchito malipengawa mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale.