Numeri 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Simiyoni anali Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai.