Numeri 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno gulu la mafuko atatu la ana a Efuraimu linanyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Elisama,+ mwana wa Amihudi.
22 Ndiyeno gulu la mafuko atatu la ana a Efuraimu linanyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Elisama,+ mwana wa Amihudi.