Numeri 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Manase anali Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.