Numeri 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati mungapite nafe limodzi,+ madalitso amene Yehova adzatipatse inunso mudzalandira nawo.”