Numeri 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nthawi zonse Likasa likamanyamuka, Mose ankanena kuti: “Nyamukani, inu Yehova,+ adani anu abalalike. Ndipo amene amadana nanu athawe pamaso panu.”
35 Nthawi zonse Likasa likamanyamuka, Mose ankanena kuti: “Nyamukani, inu Yehova,+ adani anu abalalike. Ndipo amene amadana nanu athawe pamaso panu.”