Numeri 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma anthuwo atayamba kulirira Mose, iye anapembedzera Yehova+ ndipo motowo unazima.