Numeri 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthuwo ankamwazikana kukatola manawo. Akatero, ankawapera pamphero kapena kuwasinja mumtondo. Kenako ankawawiritsa mumphika, kapena kuwapanga makeke ozungulira+ ndipo ankakoma ngati keke yotsekemera yothira mafuta.
8 Anthuwo ankamwazikana kukatola manawo. Akatero, ankawapera pamphero kapena kuwasinja mumtondo. Kenako ankawawiritsa mumphika, kapena kuwapanga makeke ozungulira+ ndipo ankakoma ngati keke yotsekemera yothira mafuta.