Numeri 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandivutitsa chonchi ine mtumiki wanu? Nʼchifukwa chiyani mwandiumira mtima chonchi, nʼkundisenzetsa chimtolo cha anthu onsewa?+
11 Ndiyeno Mose anauza Yehova kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandivutitsa chonchi ine mtumiki wanu? Nʼchifukwa chiyani mwandiumira mtima chonchi, nʼkundisenzetsa chimtolo cha anthu onsewa?+