Numeri 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Mose anati: “Amuna amene ndikuyenda nawo alipo 600,000,+ koma inu mwanena kuti, ‘Ndiwapatsa nyama yokwanira kudya mwezi wonse wathunthu.’
21 Ndiyeno Mose anati: “Amuna amene ndikuyenda nawo alipo 600,000,+ koma inu mwanena kuti, ‘Ndiwapatsa nyama yokwanira kudya mwezi wonse wathunthu.’