Numeri 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Choncho Mose anapita kukauza anthuwo mawu a Yehova. Iye anasonkhanitsa amuna 70 kuchokera pakati pa akulu a anthuwo, nʼkuwauza kuti aimirire mozungulira chihema chokumanako.+
24 Choncho Mose anapita kukauza anthuwo mawu a Yehova. Iye anasonkhanitsa amuna 70 kuchokera pakati pa akulu a anthuwo, nʼkuwauza kuti aimirire mozungulira chihema chokumanako.+