-
Numeri 11:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndiyeno panali amuna awiri amene anatsalira mumsasa. Mayina awo anali Eledadi ndi Medadi. Amenewanso analandira mzimuwo chifukwa anali mʼgulu la anthu amene analembedwa mayina, koma sanapite nawo kuchihema. Choncho iwonso anayamba kuchita zinthu ngati aneneri mumsasamo.
-