-
Numeri 11:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Koma Mose anayankha kuti: “Kodi ukuchita nsanje chifukwa chondidera nkhawa? Ayi usatero. Ndikanakonda anthu onse a Yehova akanakhala aneneri komanso Yehova akanaika mzimu wake pa iwo!”
-