Numeri 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma sindinachite zimenezo ndi mtumiki wanga Mose. Ndaika anthu anga onse Aisiraeli mʼmanja mwake.*+
7 Koma sindinachite zimenezo ndi mtumiki wanga Mose. Ndaika anthu anga onse Aisiraeli mʼmanja mwake.*+