Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?” Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:8 Nsanja ya Olonda,5/15/1988, tsa. 22
8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”