Numeri 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera kwambiri.+ Kenako Aroni atatembenuka nʼkumuyangʼana Miriamu, anaona kuti wachita khate.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:10 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 26
10 Mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera kwambiri.+ Kenako Aroni atatembenuka nʼkumuyangʼana Miriamu, anaona kuti wachita khate.+