Numeri 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova anauza Mose kuti: “Kodi bambo ake akanamulavulira malovu kumaso, sakanakhala wonyozeka kwa masiku 7? Ndiye mʼtulutseni akakhale kunja kwa msasa+ kwa masiku 7, pambuyo pake mumulowetsenso mumsasamo.”
14 Yehova anauza Mose kuti: “Kodi bambo ake akanamulavulira malovu kumaso, sakanakhala wonyozeka kwa masiku 7? Ndiye mʼtulutseni akakhale kunja kwa msasa+ kwa masiku 7, pambuyo pake mumulowetsenso mumsasamo.”