Numeri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa kwa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke mpaka Miriamu atamubweretsanso mumsasa.
15 Choncho Miriamu anatulutsidwa kukakhala kunja kwa msasa kwa masiku 7,+ ndipo anthuwo sanasamuke mpaka Miriamu atamubweretsanso mumsasa.