Numeri 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mayina a amuna amene Mose anawatuma kuti akazonde dzikolo ndi amenewa. Mose anapatsa Hoshiya mwana wa Nuni dzina lakuti Yoswa.*+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:16 Nsanja ya Olonda,12/1/2002, tsa. 1112/15/1986, tsa. 14
16 Mayina a amuna amene Mose anawatuma kuti akazonde dzikolo ndi amenewa. Mose anapatsa Hoshiya mwana wa Nuni dzina lakuti Yoswa.*+