Numeri 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mukaone kuti dzikolo ndi lotani.+ Mukaonenso ngati anthu amʼdzikomo ndi amphamvu kapena opanda mphamvu, ngati ali ochepa kapena ambiri.
18 Mukaone kuti dzikolo ndi lotani.+ Mukaonenso ngati anthu amʼdzikomo ndi amphamvu kapena opanda mphamvu, ngati ali ochepa kapena ambiri.