Numeri 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni kumene kunkakhala Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ omwe ndi Aanaki.*+ Mzinda wa Heburoni unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani wa ku Iguputo usanamangidwe.
22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni kumene kunkakhala Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ omwe ndi Aanaki.*+ Mzinda wa Heburoni unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani wa ku Iguputo usanamangidwe.