Numeri 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako gulu lonselo linayamba kudandaula mofuula, ndipo anthuwo anapitiriza kulira usiku wonse.+