Numeri 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anauza gulu lonse la Aisiraeli kuti: “Dziko limene tinakalowamo nʼkulizonda ndi dziko labwino kwambiri.+
7 Iwo anauza gulu lonse la Aisiraeli kuti: “Dziko limene tinakalowamo nʼkulizonda ndi dziko labwino kwambiri.+