Numeri 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ana anu adzakhala abusa mʼchipululu kwa zaka 40,+ ndipo adzavutika chifukwa cha kusakhulupirika kwanu,* mpaka womalizira kufa wa inu atagona mʼmanda mʼchipululu muno.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:33 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, ptsa. 30-31
33 Ana anu adzakhala abusa mʼchipululu kwa zaka 40,+ ndipo adzavutika chifukwa cha kusakhulupirika kwanu,* mpaka womalizira kufa wa inu atagona mʼmanda mʼchipululu muno.+