Numeri 14:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kumeneko mukakumana ndi Aamaleki komanso Akanani,+ ndipo akakuphani ndi lupanga. Yehova sapita nanu kumeneko chifukwa mwasiya kutsatira Yehova.”+
43 Kumeneko mukakumana ndi Aamaleki komanso Akanani,+ ndipo akakuphani ndi lupanga. Yehova sapita nanu kumeneko chifukwa mwasiya kutsatira Yehova.”+