Numeri 14:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Komabe anthuwo anadzikuza ndipo ananyamuka nʼkupita kudera lamapiri kuja,+ koma Mose limodzi ndi likasa la pangano la Yehova sanachoke pakati pa msasa.+
44 Komabe anthuwo anadzikuza ndipo ananyamuka nʼkupita kudera lamapiri kuja,+ koma Mose limodzi ndi likasa la pangano la Yehova sanachoke pakati pa msasa.+