Numeri 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 munthu amene akuperekayo azikapereka ngʼombe yamphongoyo limodzi ndi nsembe yambewu.+ Nsembe yambewuyo izikakhala yokwana magawo atatu a magawo 10 a ufa wosalala a muyezo wa efa. Ufawo azikauthira mafuta okwana hafu ya muyezo wa hini.
9 munthu amene akuperekayo azikapereka ngʼombe yamphongoyo limodzi ndi nsembe yambewu.+ Nsembe yambewuyo izikakhala yokwana magawo atatu a magawo 10 a ufa wosalala a muyezo wa efa. Ufawo azikauthira mafuta okwana hafu ya muyezo wa hini.