Numeri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu amene ndinu mpingo wa Isiraeli komanso mlendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo ofanana. Muzitsatira malamulo amenewa mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale, mlendo komanso inuyo nʼchimodzimodzi pamaso pa Yehova.+
15 Inu amene ndinu mpingo wa Isiraeli komanso mlendo amene akukhala pakati panu, mukhale ndi malamulo ofanana. Muzitsatira malamulo amenewa mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale, mlendo komanso inuyo nʼchimodzimodzi pamaso pa Yehova.+