Numeri 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 muzikapereka chopereka kwa Yehova pa chakudya chilichonse chamʼdzikolo,+ chimene muzikadya.