Numeri 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Si izi nanga, sunatifikitse kudziko lililonse loyenda mkaka ndi uchi+ kapena kutipatsa malo ndiponso minda ya mpesa. Kodi ukufuna kuti amunawo uwakolowole maso? Tatitu kumeneko sitibwerako!”
14 Si izi nanga, sunatifikitse kudziko lililonse loyenda mkaka ndi uchi+ kapena kutipatsa malo ndiponso minda ya mpesa. Kodi ukufuna kuti amunawo uwakolowole maso? Tatitu kumeneko sitibwerako!”